Upandu mu Ndakatulo: “Anyamata Awiri Akufa”
Tsiku lina lowala pakati pa usiku, anyamata awiri akufa anadzuka kuti amenyane. Kubwerera chammbuyo iwo anayang'anizana wina ndi mzake, anasolola malupanga awo ndipo anawomberana wina ndi mzake